Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 24 - الزُّخرُف - Page - Juz 25
﴿۞ قَٰلَ أَوَلَوۡ جِئۡتُكُم بِأَهۡدَىٰ مِمَّا وَجَدتُّمۡ عَلَيۡهِ ءَابَآءَكُمۡۖ قَالُوٓاْ إِنَّا بِمَآ أُرۡسِلۡتُم بِهِۦ كَٰفِرُونَ ﴾
[الزُّخرُف: 24]
﴿قال أو لو جئتكم بأهدى مما وجدتم عليه آباءكم قالوا إنا بما﴾ [الزُّخرُف: 24]
Khaled Ibrahim Betala “Adanena (mneneri wawo): “Ngakhale ndakubweretserani chipembedzo chabwino kuposa chomwe mudawapeza nacho makolo anu (mupitirizabe kutsatira chipembedzo cha makolo anucho)?” Adanena: “Ife tikuzikana zimene mwatumidwa nazozi.” |