Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 58 - الزُّخرُف - Page - Juz 25
﴿وَقَالُوٓاْ ءَأَٰلِهَتُنَا خَيۡرٌ أَمۡ هُوَۚ مَا ضَرَبُوهُ لَكَ إِلَّا جَدَلَۢاۚ بَلۡ هُمۡ قَوۡمٌ خَصِمُونَ ﴾
[الزُّخرُف: 58]
﴿وقالوا أآلهتنا خير أم هو ما ضربوه لك إلا جدلا بل هم﴾ [الزُّخرُف: 58]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo adati: “Kodi milungu yathu ndi yabwino, kapena iye?” Sadamfanizire kwa iwe koma kufuna kutsutsana basi (kopanda kufuna choona). Koma iwo ndi anthu amtsutso |