×

Mbale za golide ndi zikho zomwera zidzaperekedwa kwa iwo ndipo mu izo 43:71 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zukhruf ⮕ (43:71) ayat 71 in Chichewa

43:71 Surah Az-Zukhruf ayat 71 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 71 - الزُّخرُف - Page - Juz 25

﴿يُطَافُ عَلَيۡهِم بِصِحَافٖ مِّن ذَهَبٖ وَأَكۡوَابٖۖ وَفِيهَا مَا تَشۡتَهِيهِ ٱلۡأَنفُسُ وَتَلَذُّ ٱلۡأَعۡيُنُۖ وَأَنتُمۡ فِيهَا خَٰلِدُونَ ﴾
[الزُّخرُف: 71]

Mbale za golide ndi zikho zomwera zidzaperekedwa kwa iwo ndipo mu izo mudzakhala zimene mitima yawo inali kulakalaka ndi ponso zosangalala kuziona. Ndipo inu mudzakhala momwemo mpaka kalekale

❮ Previous Next ❯

ترجمة: يطاف عليهم بصحاف من ذهب وأكواب وفيها ما تشتهيه الأنفس وتلذ الأعين, باللغة نيانجا

﴿يطاف عليهم بصحاف من ذهب وأكواب وفيها ما تشتهيه الأنفس وتلذ الأعين﴾ [الزُّخرُف: 71]

Khaled Ibrahim Betala
“Adzakhala akupititsidwa mbale zagolide ndi matambula (agolide); zonse zokomera moyo zidzakhala mmenemo ndi zokomera maso, ndipo inu mudzakhala mmenemo nthawi yaitali
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek