Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 81 - الزُّخرُف - Page - Juz 25
﴿قُلۡ إِن كَانَ لِلرَّحۡمَٰنِ وَلَدٞ فَأَنَا۠ أَوَّلُ ٱلۡعَٰبِدِينَ ﴾
[الزُّخرُف: 81]
﴿قل إن كان للرحمن ولد فأنا أول العابدين﴾ [الزُّخرُف: 81]
Khaled Ibrahim Betala “Nena (kwa omphatikiza Allah ndi mafano): “Zikadakhala kuti (Allah) Wachifundo chambiri ali ndi mwana, ndiye kuti ine ndikadakhala woyamba kumpembedza (mwanayo).” |