Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 84 - الزُّخرُف - Page - Juz 25
﴿وَهُوَ ٱلَّذِي فِي ٱلسَّمَآءِ إِلَٰهٞ وَفِي ٱلۡأَرۡضِ إِلَٰهٞۚ وَهُوَ ٱلۡحَكِيمُ ٱلۡعَلِيمُ ﴾
[الزُّخرُف: 84]
﴿وهو الذي في السماء إله وفي الأرض إله وهو الحكيم العليم﴾ [الزُّخرُف: 84]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo Iye ndiamene akupembedzedwa kumwamba, ndiponso ndi Iye Amene akupembedzedwa pansi. Iye ndi Wanzeru zakuya, Wodziwa kwambiri |