Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 85 - الزُّخرُف - Page - Juz 25
﴿وَتَبَارَكَ ٱلَّذِي لَهُۥ مُلۡكُ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِ وَمَا بَيۡنَهُمَا وَعِندَهُۥ عِلۡمُ ٱلسَّاعَةِ وَإِلَيۡهِ تُرۡجَعُونَ ﴾
[الزُّخرُف: 85]
﴿وتبارك الذي له ملك السموات والأرض وما بينهما وعنده علم الساعة وإليه﴾ [الزُّخرُف: 85]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo watukuka kwambiri Yemwe ufumu wa kumwamba ndi pansi ndi pakati pa zimenezi ndi Wake. Ndiponso kwa Iye ndiko kuli kudziwa kudza kwa tsiku la Qiyâma; ndipo kwa Iye Yekha ndi kumene m’dzabwezedwa |