×

Ndithudi ngati iwe ukawafunsa kuti, “Kodi ndani adalenga kumwamba ndi dziko lapansi?” 43:9 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zukhruf ⮕ (43:9) ayat 9 in Chichewa

43:9 Surah Az-Zukhruf ayat 9 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 9 - الزُّخرُف - Page - Juz 25

﴿وَلَئِن سَأَلۡتَهُم مَّنۡ خَلَقَ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضَ لَيَقُولُنَّ خَلَقَهُنَّ ٱلۡعَزِيزُ ٱلۡعَلِيمُ ﴾
[الزُّخرُف: 9]

Ndithudi ngati iwe ukawafunsa kuti, “Kodi ndani adalenga kumwamba ndi dziko lapansi?” Iwo, ndithudi, adzakuyankha kuti, “Mwini mphamvu ndi Mwini wodziwa ndiye amene adazilenga.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولئن سألتهم من خلق السموات والأرض ليقولن خلقهن العزيز العليم, باللغة نيانجا

﴿ولئن سألتهم من خلق السموات والأرض ليقولن خلقهن العزيز العليم﴾ [الزُّخرُف: 9]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ukawafunsa: “Ndani adalenga thambo ndi nthaka?” Ndithu ayankha kuti: “Adazilenga (Allah) Mwini Mphamvu, Wodziwa.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek