Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 8 - الزُّخرُف - Page - Juz 25
﴿فَأَهۡلَكۡنَآ أَشَدَّ مِنۡهُم بَطۡشٗا وَمَضَىٰ مَثَلُ ٱلۡأَوَّلِينَ ﴾
[الزُّخرُف: 8]
﴿فأهلكنا أشد منهم بطشا ومضى مثل الأولين﴾ [الزُّخرُف: 8]
Khaled Ibrahim Betala “Choncho tidawaononga amene adali amphamvu kuposa iwo (Aquraish) ndipo ladutsa fanizo la (zilango zomwe zidawapeza) anthu akale |