Quran with Chichewa translation - Surah Ad-Dukhan ayat 22 - الدُّخان - Page - Juz 25
﴿فَدَعَا رَبَّهُۥٓ أَنَّ هَٰٓؤُلَآءِ قَوۡمٞ مُّجۡرِمُونَ ﴾
[الدُّخان: 22]
﴿فدعا ربه أن هؤلاء قوم مجرمون﴾ [الدُّخان: 22]
Khaled Ibrahim Betala ““(Koma adamchitira mtopola). Ndipo iye adaitana Mbuye wake kuti: “Awa ndithu ndi anthu oipa.” |