Quran with Chichewa translation - Surah Ad-Dukhan ayat 32 - الدُّخان - Page - Juz 25
﴿وَلَقَدِ ٱخۡتَرۡنَٰهُمۡ عَلَىٰ عِلۡمٍ عَلَى ٱلۡعَٰلَمِينَ ﴾
[الدُّخان: 32]
﴿ولقد اخترناهم على علم على العالمين﴾ [الدُّخان: 32]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ndithu tidawasankha (Ayuda nthawi imeneyo) pa mitundu ina m’kudziwa Kwathu |