Quran with Chichewa translation - Surah Ad-Dukhan ayat 36 - الدُّخان - Page - Juz 25
﴿فَأۡتُواْ بِـَٔابَآئِنَآ إِن كُنتُمۡ صَٰدِقِينَ ﴾
[الدُّخان: 36]
﴿فأتوا بآبائنا إن كنتم صادقين﴾ [الدُّخان: 36]
Khaled Ibrahim Betala ““Choncho tibweretsereni makolo athu (amene adafa), ngati mukunena zoona (kuti kuli kuuka).” |