Quran with Chichewa translation - Surah Ad-Dukhan ayat 49 - الدُّخان - Page - Juz 25
﴿ذُقۡ إِنَّكَ أَنتَ ٱلۡعَزِيزُ ٱلۡكَرِيمُ ﴾
[الدُّخان: 49]
﴿ذق إنك أنت العزيز الكريم﴾ [الدُّخان: 49]
Khaled Ibrahim Betala “(Adzauzidwa mwachipongwe): “Lawa! Ndithu iwe ndiwe wamphamvu zambiri, wolemekezeka, (monga momwe udali kudzitamira muja).” |