Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jathiyah ayat 13 - الجاثِية - Page - Juz 25
﴿وَسَخَّرَ لَكُم مَّا فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَمَا فِي ٱلۡأَرۡضِ جَمِيعٗا مِّنۡهُۚ إِنَّ فِي ذَٰلِكَ لَأٓيَٰتٖ لِّقَوۡمٖ يَتَفَكَّرُونَ ﴾
[الجاثِية: 13]
﴿وسخر لكم ما في السموات وما في الأرض جميعا منه إن في﴾ [الجاثِية: 13]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo wakugonjetserani za kumwamba ndi zam’nthaka, zonse zikuchokera kwa Iye. Ndithu mzimenezo muli zisonyezo kwa anthu amene amalingalira |