×

Auze iwo amene amakhulupirira kuti akhululukire iwo amene sakhulupirira m’masiku a Mulungu 45:14 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Jathiyah ⮕ (45:14) ayat 14 in Chichewa

45:14 Surah Al-Jathiyah ayat 14 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jathiyah ayat 14 - الجاثِية - Page - Juz 25

﴿قُل لِّلَّذِينَ ءَامَنُواْ يَغۡفِرُواْ لِلَّذِينَ لَا يَرۡجُونَ أَيَّامَ ٱللَّهِ لِيَجۡزِيَ قَوۡمَۢا بِمَا كَانُواْ يَكۡسِبُونَ ﴾
[الجاثِية: 14]

Auze iwo amene amakhulupirira kuti akhululukire iwo amene sakhulupirira m’masiku a Mulungu kuti Iye akhoza kulipira anthu chimene amachita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل للذين آمنوا يغفروا للذين لا يرجون أيام الله ليجزي قوما بما, باللغة نيانجا

﴿قل للذين آمنوا يغفروا للذين لا يرجون أيام الله ليجزي قوما بما﴾ [الجاثِية: 14]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena kwa amene akhulupirira kuti awakhululukire amene sakuopa masiku a Allah (a chilango; mmasiku amenewo) kuti awalipire anthu pa zomwe amachita (zoipa)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek