×

Ndipo Ife tidawapatsa zizindikiro zooneka za chipembedzo. Ndipo iwo adayamba mipatuko pamene 45:17 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Jathiyah ⮕ (45:17) ayat 17 in Chichewa

45:17 Surah Al-Jathiyah ayat 17 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jathiyah ayat 17 - الجاثِية - Page - Juz 25

﴿وَءَاتَيۡنَٰهُم بَيِّنَٰتٖ مِّنَ ٱلۡأَمۡرِۖ فَمَا ٱخۡتَلَفُوٓاْ إِلَّا مِنۢ بَعۡدِ مَا جَآءَهُمُ ٱلۡعِلۡمُ بَغۡيَۢا بَيۡنَهُمۡۚ إِنَّ رَبَّكَ يَقۡضِي بَيۡنَهُمۡ يَوۡمَ ٱلۡقِيَٰمَةِ فِيمَا كَانُواْ فِيهِ يَخۡتَلِفُونَ ﴾
[الجاثِية: 17]

Ndipo Ife tidawapatsa zizindikiro zooneka za chipembedzo. Ndipo iwo adayamba mipatuko pamene nzeru zidaperekedwa kwa iwo chifukwa cha njiru pakati pawo. Ndithudi Ambuye wako adzaweruza pakati pawo pa tsiku lachiweruzo pa nkhani zimene anali kutsutsana

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وآتيناهم بينات من الأمر فما اختلفوا إلا من بعد ما جاءهم العلم, باللغة نيانجا

﴿وآتيناهم بينات من الأمر فما اختلفوا إلا من بعد ما جاءهم العلم﴾ [الجاثِية: 17]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo tidawapatsa zisonyezo zoonekera pazinthu zachipembedzo chawo; sadapatukane mpaka pomwe kudawadzera kudziwa, chifukwa chadumbo pakati pawo. Ndithu Mbuye wako adzalamula pakati pawo tsiku la Qiyâma pa zimene adali kutsemphana
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek