×

Ndipo iwe takuika pa njira yoyenera. Motero tsatira yoyenerayo ndipo usatsatire zilakolako 45:18 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Jathiyah ⮕ (45:18) ayat 18 in Chichewa

45:18 Surah Al-Jathiyah ayat 18 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jathiyah ayat 18 - الجاثِية - Page - Juz 25

﴿ثُمَّ جَعَلۡنَٰكَ عَلَىٰ شَرِيعَةٖ مِّنَ ٱلۡأَمۡرِ فَٱتَّبِعۡهَا وَلَا تَتَّبِعۡ أَهۡوَآءَ ٱلَّذِينَ لَا يَعۡلَمُونَ ﴾
[الجاثِية: 18]

Ndipo iwe takuika pa njira yoyenera. Motero tsatira yoyenerayo ndipo usatsatire zilakolako za iwo amene sadziwa chilichonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ثم جعلناك على شريعة من الأمر فاتبعها ولا تتبع أهواء الذين لا, باللغة نيانجا

﴿ثم جعلناك على شريعة من الأمر فاتبعها ولا تتبع أهواء الذين لا﴾ [الجاثِية: 18]

Khaled Ibrahim Betala
“Kenako tidakuika iwe pa malamulo a zinthu za chipembedzo (Chathu). Choncho tsatira malamulo (Athu), ndipo usatsate zilakolako za amene sadziwa (njira yoona)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek