Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jathiyah ayat 20 - الجاثِية - Page - Juz 25
﴿هَٰذَا بَصَٰٓئِرُ لِلنَّاسِ وَهُدٗى وَرَحۡمَةٞ لِّقَوۡمٖ يُوقِنُونَ ﴾
[الجاثِية: 20]
﴿هذا بصائر للناس وهدى ورحمة لقوم يوقنون﴾ [الجاثِية: 20]
Khaled Ibrahim Betala “Iyi (Qur’an imene yavumbulutsidwa kwa iwe), ndizisonyezo kwa anthu chiongoko ndi chifundo kwa anthu omwe akutsimikiza (kuti lilipo tsiku la chiweruziro) |