Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jathiyah ayat 22 - الجاثِية - Page - Juz 25
﴿وَخَلَقَ ٱللَّهُ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضَ بِٱلۡحَقِّ وَلِتُجۡزَىٰ كُلُّ نَفۡسِۭ بِمَا كَسَبَتۡ وَهُمۡ لَا يُظۡلَمُونَ ﴾
[الجاثِية: 22]
﴿وخلق الله السموات والأرض بالحق ولتجزى كل نفس بما كسبت وهم لا﴾ [الجاثِية: 22]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo Allah adalenga thambo ndi nthaka moona ndi kuti mzimu uliwonse ulipidwe zimene udadzichitira, (zoipa kapena zabwino) ndipo iwo sadzaponderezedwa |