×

Koma iwo amene sadakhulupirire adzauzidwa kuti, “Kodi chivumbulutso changa sichidalakatulidwe kwa inu? 45:31 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Jathiyah ⮕ (45:31) ayat 31 in Chichewa

45:31 Surah Al-Jathiyah ayat 31 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jathiyah ayat 31 - الجاثِية - Page - Juz 25

﴿وَأَمَّا ٱلَّذِينَ كَفَرُوٓاْ أَفَلَمۡ تَكُنۡ ءَايَٰتِي تُتۡلَىٰ عَلَيۡكُمۡ فَٱسۡتَكۡبَرۡتُمۡ وَكُنتُمۡ قَوۡمٗا مُّجۡرِمِينَ ﴾
[الجاثِية: 31]

Koma iwo amene sadakhulupirire adzauzidwa kuti, “Kodi chivumbulutso changa sichidalakatulidwe kwa inu? Koma inu munali onyada ndipo munali anthu ochita zoipa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وأما الذين كفروا أفلم تكن آياتي تتلى عليكم فاستكبرتم وكنتم قوما مجرمين, باللغة نيانجا

﴿وأما الذين كفروا أفلم تكن آياتي تتلى عليكم فاستكبرتم وكنتم قوما مجرمين﴾ [الجاثِية: 31]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo amene adakanira, (adzauzidwa kuti): “Kodi Ayah Zanga sizidali kuwerengedwa kwa inu? Koma inu mudadzikweza; ndipo mudali anthu oipa.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek