×

Ndipo iwo amene adakhulupirira ndipo amachita ntchito zabwino, Ambuye wawo adzawalowetsa m’chisomo 45:30 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Jathiyah ⮕ (45:30) ayat 30 in Chichewa

45:30 Surah Al-Jathiyah ayat 30 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jathiyah ayat 30 - الجاثِية - Page - Juz 25

﴿فَأَمَّا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَعَمِلُواْ ٱلصَّٰلِحَٰتِ فَيُدۡخِلُهُمۡ رَبُّهُمۡ فِي رَحۡمَتِهِۦۚ ذَٰلِكَ هُوَ ٱلۡفَوۡزُ ٱلۡمُبِينُ ﴾
[الجاثِية: 30]

Ndipo iwo amene adakhulupirira ndipo amachita ntchito zabwino, Ambuye wawo adzawalowetsa m’chisomo chake. Kumeneku ndiko kupambana kwenikweni

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فأما الذين آمنوا وعملوا الصالحات فيدخلهم ربهم في رحمته ذلك هو الفوز, باللغة نيانجا

﴿فأما الذين آمنوا وعملوا الصالحات فيدخلهم ربهم في رحمته ذلك هو الفوز﴾ [الجاثِية: 30]

Khaled Ibrahim Betala
“Koma amene adakhulupirira ndi kuchita zabwino, Mbuye wawo adzawalowetsa ku chifundo Chake; kumeneko ndiko kupambana koonekera
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek