×

“Ichi ndi chifukwa chakuti mudatenga chivumbulutso cha Mulungu ngati chinthu choseweretsa ndipo 45:35 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Jathiyah ⮕ (45:35) ayat 35 in Chichewa

45:35 Surah Al-Jathiyah ayat 35 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jathiyah ayat 35 - الجاثِية - Page - Juz 25

﴿ذَٰلِكُم بِأَنَّكُمُ ٱتَّخَذۡتُمۡ ءَايَٰتِ ٱللَّهِ هُزُوٗا وَغَرَّتۡكُمُ ٱلۡحَيَوٰةُ ٱلدُّنۡيَاۚ فَٱلۡيَوۡمَ لَا يُخۡرَجُونَ مِنۡهَا وَلَا هُمۡ يُسۡتَعۡتَبُونَ ﴾
[الجاثِية: 35]

“Ichi ndi chifukwa chakuti mudatenga chivumbulutso cha Mulungu ngati chinthu choseweretsa ndipo moyo wa padziko lino lapansi udakunyengani inu.” Motero patsiku limeneli, iwo sadzachotsedwa ndipo sadzaloledwa kukonza zolakwa zawo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ذلكم بأنكم اتخذتم آيات الله هزوا وغرتكم الحياة الدنيا فاليوم لا يخرجون, باللغة نيانجا

﴿ذلكم بأنكم اتخذتم آيات الله هزوا وغرتكم الحياة الدنيا فاليوم لا يخرجون﴾ [الجاثِية: 35]

Khaled Ibrahim Betala
““Zimenezi nchifukwa chakuti inu mudazichitira chipongwe Ayah za Allah, ndipo moyo wa pa dziko udakunyengani.” Choncho lero satulutsidwa mmenemo ndipo madandaulo awo savomerezedwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek