×

Ndipo kudzanenedwa kuti, “Lero takuiwalani inu monga momwe inu mudaiwalira za tsiku 45:34 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Jathiyah ⮕ (45:34) ayat 34 in Chichewa

45:34 Surah Al-Jathiyah ayat 34 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jathiyah ayat 34 - الجاثِية - Page - Juz 25

﴿وَقِيلَ ٱلۡيَوۡمَ نَنسَىٰكُمۡ كَمَا نَسِيتُمۡ لِقَآءَ يَوۡمِكُمۡ هَٰذَا وَمَأۡوَىٰكُمُ ٱلنَّارُ وَمَا لَكُم مِّن نَّٰصِرِينَ ﴾
[الجاثِية: 34]

Ndipo kudzanenedwa kuti, “Lero takuiwalani inu monga momwe inu mudaiwalira za tsiku lanuli. Ndipo malo anu okhala ndi ku Moto ndipo kumeneko sikudzakhala wina wokuthandizani.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقيل اليوم ننساكم كما نسيتم لقاء يومكم هذا ومأواكم النار وما لكم, باللغة نيانجا

﴿وقيل اليوم ننساكم كما نسيتم لقاء يومكم هذا ومأواكم النار وما لكم﴾ [الجاثِية: 34]

Khaled Ibrahim Betala
“Kudzanenedwanso kwa iwowa: “Lero tikuiwalani (pokusiyani mchilango) monga momwe inu mudaiwalira kukumana ndi tsiku lanu ili. Ndipo malo anu ndi ku Moto, ndipo mulibe wokupulumutsani.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek