×

Iwo adati, “oh inu anthu athu! Ife tamva mawu a m’Buku limene 46:30 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahqaf ⮕ (46:30) ayat 30 in Chichewa

46:30 Surah Al-Ahqaf ayat 30 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahqaf ayat 30 - الأحقَاف - Page - Juz 26

﴿قَالُواْ يَٰقَوۡمَنَآ إِنَّا سَمِعۡنَا كِتَٰبًا أُنزِلَ مِنۢ بَعۡدِ مُوسَىٰ مُصَدِّقٗا لِّمَا بَيۡنَ يَدَيۡهِ يَهۡدِيٓ إِلَى ٱلۡحَقِّ وَإِلَىٰ طَرِيقٖ مُّسۡتَقِيمٖ ﴾
[الأحقَاف: 30]

Iwo adati, “oh inu anthu athu! Ife tamva mawu a m’Buku limene lavumbulutsidwa pambuyo pa Mose limene litsimikizira zimene zidavumbulutsidwa kale zotsogolera anthu ku choonadi ndi kunjira yoyenera.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قالوا ياقومنا إنا سمعنا كتابا أنـزل من بعد موسى مصدقا لما بين, باللغة نيانجا

﴿قالوا ياقومنا إنا سمعنا كتابا أنـزل من بعد موسى مصدقا لما بين﴾ [الأحقَاف: 30]

Khaled Ibrahim Betala
“Zidanena: “E inu anzathu! Ife tamva (zowerengedwa) za m’buku (lolemekezeka) lomwe lavumbulutsidwa pambuyo pa Mûsa, loikira umboni zimene zidalitsogolera; likuongolera ku choona ndi kunjira yolunjika.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek