×

Ndi pamene Ife tidatumiza kwa iwe, gulu la majini limene lidadzamvetsera Korani, 46:29 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahqaf ⮕ (46:29) ayat 29 in Chichewa

46:29 Surah Al-Ahqaf ayat 29 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahqaf ayat 29 - الأحقَاف - Page - Juz 26

﴿وَإِذۡ صَرَفۡنَآ إِلَيۡكَ نَفَرٗا مِّنَ ٱلۡجِنِّ يَسۡتَمِعُونَ ٱلۡقُرۡءَانَ فَلَمَّا حَضَرُوهُ قَالُوٓاْ أَنصِتُواْۖ فَلَمَّا قُضِيَ وَلَّوۡاْ إِلَىٰ قَوۡمِهِم مُّنذِرِينَ ﴾
[الأحقَاف: 29]

Ndi pamene Ife tidatumiza kwa iwe, gulu la majini limene lidadzamvetsera Korani, ndipo pamene iwo adaimirira pakati pawo adati, “Khalani chete!” Ndipo pamene atatha kumvetsera, iwo adabwerera kwa anthu awo ngati ochenjeza

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذ صرفنا إليك نفرا من الجن يستمعون القرآن فلما حضروه قالوا أنصتوا, باللغة نيانجا

﴿وإذ صرفنا إليك نفرا من الجن يستمعون القرآن فلما حضروه قالوا أنصتوا﴾ [الأحقَاف: 29]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (kumbuka iwe Mtumiki{s.a.w}) pamene tidakutumizira gulu la ziwanda (majini) kudzamvera Qur’an ndipo pamene izo zidafika pamalopo zidanena pakati pawo: “Khalani chete!” Pomwe kuwerenga (kwa Qur’an) kudatha, zidabwerera ku mtundu wawo kukawachenjeza (za chilango cha Allah)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek