×

Kodi iwo saona kuti Mulungu, amene adalenga kumwamba ndi dziko lapansi, sadatope 46:33 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahqaf ⮕ (46:33) ayat 33 in Chichewa

46:33 Surah Al-Ahqaf ayat 33 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahqaf ayat 33 - الأحقَاف - Page - Juz 26

﴿أَوَلَمۡ يَرَوۡاْ أَنَّ ٱللَّهَ ٱلَّذِي خَلَقَ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضَ وَلَمۡ يَعۡيَ بِخَلۡقِهِنَّ بِقَٰدِرٍ عَلَىٰٓ أَن يُحۡـِۧيَ ٱلۡمَوۡتَىٰۚ بَلَىٰٓۚ إِنَّهُۥ عَلَىٰ كُلِّ شَيۡءٖ قَدِيرٞ ﴾
[الأحقَاف: 33]

Kodi iwo saona kuti Mulungu, amene adalenga kumwamba ndi dziko lapansi, sadatope chifukwa cha ntchito yolengayi ndipo kuti ali ndi mphamvu yopereka moyo kwa akufa? Inde! Ndithudi Iye ali ndi mphamvu pa chinthu china chilichonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أو لم يروا أن الله الذي خلق السموات والأرض ولم يعي بخلقهن, باللغة نيانجا

﴿أو لم يروا أن الله الذي خلق السموات والأرض ولم يعي بخلقهن﴾ [الأحقَاف: 33]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi iwo saona kuti Allah Amene adalenga thambo ndi nthaka, ndipo sadatope pozilenga, ndi Wakutha kuwaukitsa anthu ku irnfa? Inde, ndithu Iye Ngokhoza kuchita chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek