×

Ngati wina safuna kumvera Mtumwi wa Mulungu, iye sadzathawa sadzathawa chikonzero cha 46:32 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahqaf ⮕ (46:32) ayat 32 in Chichewa

46:32 Surah Al-Ahqaf ayat 32 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahqaf ayat 32 - الأحقَاف - Page - Juz 26

﴿وَمَن لَّا يُجِبۡ دَاعِيَ ٱللَّهِ فَلَيۡسَ بِمُعۡجِزٖ فِي ٱلۡأَرۡضِ وَلَيۡسَ لَهُۥ مِن دُونِهِۦٓ أَوۡلِيَآءُۚ أُوْلَٰٓئِكَ فِي ضَلَٰلٖ مُّبِينٍ ﴾
[الأحقَاف: 32]

Ngati wina safuna kumvera Mtumwi wa Mulungu, iye sadzathawa sadzathawa chikonzero cha Mulungu cha padziko lapansi ndipo sadzapeza wina womuteteza kupatula Mulungu. otere ndi olakwa kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ومن لا يجب داعي الله فليس بمعجز في الأرض وليس له من, باللغة نيانجا

﴿ومن لا يجب داعي الله فليس بمعجز في الأرض وليس له من﴾ [الأحقَاف: 32]

Khaled Ibrahim Betala
“Ngati wina samuvomera woitanira kwa Allah, sangamulepheretse (Allah) pa dziko (akafuna kumuchita kanthu), ndipo iye alibe atetezi ena kupatula Iye (Allah). Otere akusokera koonekera poyera.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek