×

Ndipo pamene chivumbulutso chathu chomveka chimawerengedwa kwa iwo, anthu osakhulupirira amanena za 46:7 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahqaf ⮕ (46:7) ayat 7 in Chichewa

46:7 Surah Al-Ahqaf ayat 7 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahqaf ayat 7 - الأحقَاف - Page - Juz 26

﴿وَإِذَا تُتۡلَىٰ عَلَيۡهِمۡ ءَايَٰتُنَا بَيِّنَٰتٖ قَالَ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ لِلۡحَقِّ لَمَّا جَآءَهُمۡ هَٰذَا سِحۡرٞ مُّبِينٌ ﴾
[الأحقَاف: 7]

Ndipo pamene chivumbulutso chathu chomveka chimawerengedwa kwa iwo, anthu osakhulupirira amanena za choonadi pamene chidza kwa iwo kuti “Awa ndi matsenga oonekera poyera.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا تتلى عليهم آياتنا بينات قال الذين كفروا للحق لما جاءهم هذا, باللغة نيانجا

﴿وإذا تتلى عليهم آياتنا بينات قال الذين كفروا للحق لما جاءهم هذا﴾ [الأحقَاف: 7]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo pamene zikuwerengedwa kwa iwo Ayah Zathu zolongosola chilichonse (cha m’chipembedzo), amene sadakhulupirire amanena pa choonadi chikawadzera: “Awa ndi matsenga oonekera.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek