Quran with Chichewa translation - Surah Al-Fath ayat 19 - الفَتح - Page - Juz 26
﴿وَمَغَانِمَ كَثِيرَةٗ يَأۡخُذُونَهَاۗ وَكَانَ ٱللَّهُ عَزِيزًا حَكِيمٗا ﴾
[الفَتح: 19]
﴿ومغانم كثيرة يأخذونها وكان الله عزيزا حكيما﴾ [الفَتح: 19]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo zofunkha zambiri za pa nkhondo adzazitenga; ndipo Allah Ngwamphamvu zoposa, Wanzeru zakuya |