Quran with Chichewa translation - Surah Al-Fath ayat 24 - الفَتح - Page - Juz 26
﴿وَهُوَ ٱلَّذِي كَفَّ أَيۡدِيَهُمۡ عَنكُمۡ وَأَيۡدِيَكُمۡ عَنۡهُم بِبَطۡنِ مَكَّةَ مِنۢ بَعۡدِ أَنۡ أَظۡفَرَكُمۡ عَلَيۡهِمۡۚ وَكَانَ ٱللَّهُ بِمَا تَعۡمَلُونَ بَصِيرًا ﴾
[الفَتح: 24]
﴿وهو الذي كف أيديهم عنكم وأيديكم عنهم ببطن مكة من بعد أن﴾ [الفَتح: 24]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo Iye ndi amene adatsekereza manja awo pa inu; ndi manja anu pa iwo, pa chigwa cha Makka, pambuyo pokupambanitsani pa iwo. Ndipo Allah akuona zonse zimene mukuchita |