Quran with Chichewa translation - Surah Al-Fath ayat 8 - الفَتح - Page - Juz 26
﴿إِنَّآ أَرۡسَلۡنَٰكَ شَٰهِدٗا وَمُبَشِّرٗا وَنَذِيرٗا ﴾
[الفَتح: 8]
﴿إنا أرسلناك شاهدا ومبشرا ونذيرا﴾ [الفَتح: 8]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu takutumiza kuti ukhale mboni ndi wolengeza nkhani zabwino ndiponso mchenjezi |