×

Nena, “Kodi inu mungamuphunzitse Mulungu za chipembedzo chanu? Pamene Mulungu amadziwa chilichonse 49:16 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hujurat ⮕ (49:16) ayat 16 in Chichewa

49:16 Surah Al-hujurat ayat 16 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hujurat ayat 16 - الحُجُرَات - Page - Juz 26

﴿قُلۡ أَتُعَلِّمُونَ ٱللَّهَ بِدِينِكُمۡ وَٱللَّهُ يَعۡلَمُ مَا فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَمَا فِي ٱلۡأَرۡضِۚ وَٱللَّهُ بِكُلِّ شَيۡءٍ عَلِيمٞ ﴾
[الحُجُرَات: 16]

Nena, “Kodi inu mungamuphunzitse Mulungu za chipembedzo chanu? Pamene Mulungu amadziwa chilichonse chili mlengalenga ndi padziko lapansi. Ndipo Mulungundi wodziwa chilichonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل أتعلمون الله بدينكم والله يعلم ما في السموات وما في الأرض, باللغة نيانجا

﴿قل أتعلمون الله بدينكم والله يعلم ما في السموات وما في الأرض﴾ [الحُجُرَات: 16]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Kodi mukumdziwitsa Allah za chipembedzo chanu? Koma chikhalirecho Allah akudziwa zonse za kumwamba ndi za m’dziko lapansi. Ndipo Allah Ngodziwa chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek