×

Iwo amaganiza kuti ali kukuchitira iwe chisoni pamene alowa Chisilamu. Nena, “Inu 49:17 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hujurat ⮕ (49:17) ayat 17 in Chichewa

49:17 Surah Al-hujurat ayat 17 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hujurat ayat 17 - الحُجُرَات - Page - Juz 26

﴿يَمُنُّونَ عَلَيۡكَ أَنۡ أَسۡلَمُواْۖ قُل لَّا تَمُنُّواْ عَلَيَّ إِسۡلَٰمَكُمۖ بَلِ ٱللَّهُ يَمُنُّ عَلَيۡكُمۡ أَنۡ هَدَىٰكُمۡ لِلۡإِيمَٰنِ إِن كُنتُمۡ صَٰدِقِينَ ﴾
[الحُجُرَات: 17]

Iwo amaganiza kuti ali kukuchitira iwe chisoni pamene alowa Chisilamu. Nena, “Inu simuli kundichitira ine chisoni polowa chisilamu. Iyayi, koma ndi Mulungu amene wakuchitirani inu chisoni pokulangizani njira yoyenera ngati inu, muli anthu olungama.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: يمنون عليك أن أسلموا قل لا تمنوا علي إسلامكم بل الله يمن, باللغة نيانجا

﴿يمنون عليك أن أسلموا قل لا تمنوا علي إسلامكم بل الله يمن﴾ [الحُجُرَات: 17]

Khaled Ibrahim Betala
“Akukukumba iwe chifukwa cha kulowa kwawo m’Chisilamu (ngati kuti akuchitira ufulu). Nena: “Kulowa kwanu m’Chisilamu musakuyese kuti mwandichitira ine ubwino, koma Allah ndiAmene wakuchitirani ubwino pokuongolerani ku chikhulupiliro, ngati muli owona.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek