Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 29 - المَائدة - Page - Juz 6
﴿إِنِّيٓ أُرِيدُ أَن تَبُوٓأَ بِإِثۡمِي وَإِثۡمِكَ فَتَكُونَ مِنۡ أَصۡحَٰبِ ٱلنَّارِۚ وَذَٰلِكَ جَزَٰٓؤُاْ ٱلظَّٰلِمِينَ ﴾
[المَائدة: 29]
﴿إني أريد أن تبوء بإثمي وإثمك فتكون من أصحاب النار وذلك جزاء﴾ [المَائدة: 29]
Khaled Ibrahim Betala ““Ine ndikufuna kuti usenze machimo anga pamodzi ndi machimo ako, choncho ukakhale m’gulu la anthu a ku Moto. Ndipo awo ndio malipiro a anthu ochita zoipa.” |