×

Ndipo ngati inu muitanira mapemphero, iwo amaganiza kuti ndi nthabwala ndiponso chinthu 5:58 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:58) ayat 58 in Chichewa

5:58 Surah Al-Ma’idah ayat 58 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 58 - المَائدة - Page - Juz 6

﴿وَإِذَا نَادَيۡتُمۡ إِلَى ٱلصَّلَوٰةِ ٱتَّخَذُوهَا هُزُوٗا وَلَعِبٗاۚ ذَٰلِكَ بِأَنَّهُمۡ قَوۡمٞ لَّا يَعۡقِلُونَ ﴾
[المَائدة: 58]

Ndipo ngati inu muitanira mapemphero, iwo amaganiza kuti ndi nthabwala ndiponso chinthu choseweretsa chifukwa iwo ndi anthu opanda nzeru

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا ناديتم إلى الصلاة اتخذوها هزوا ولعبا ذلك بأنهم قوم لا يعقلون, باللغة نيانجا

﴿وإذا ناديتم إلى الصلاة اتخذوها هزوا ولعبا ذلك بأنهم قوم لا يعقلون﴾ [المَائدة: 58]

Khaled Ibrahim Betala
“Mukaitanira kokapemphera Swala (mukachita azana) akuichitira chipongwe ndi masewera; ndithudi zimenezo nchifukwa chakuti iwo ndianthu opanda nzeru
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek