×

Kodi ndi chifukwa chiyani Abusa ndiponso anthu oyera, sawaletsa anthu kulankhula mawu 5:63 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:63) ayat 63 in Chichewa

5:63 Surah Al-Ma’idah ayat 63 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 63 - المَائدة - Page - Juz 6

﴿لَوۡلَا يَنۡهَىٰهُمُ ٱلرَّبَّٰنِيُّونَ وَٱلۡأَحۡبَارُ عَن قَوۡلِهِمُ ٱلۡإِثۡمَ وَأَكۡلِهِمُ ٱلسُّحۡتَۚ لَبِئۡسَ مَا كَانُواْ يَصۡنَعُونَ ﴾
[المَائدة: 63]

Kodi ndi chifukwa chiyani Abusa ndiponso anthu oyera, sawaletsa anthu kulankhula mawu amachimo kapena kudya zinthu zoletsedwa? Ndithudi zoipa ndi zimene iwo akhala ali kuchita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لولا ينهاهم الربانيون والأحبار عن قولهم الإثم وأكلهم السحت لبئس ما كانوا, باللغة نيانجا

﴿لولا ينهاهم الربانيون والأحبار عن قولهم الإثم وأكلهم السحت لبئس ما كانوا﴾ [المَائدة: 63]

Khaled Ibrahim Betala
“Bwanji odziwa za malamulo ndi akuluakulu a chipembedzo sadawaletse zoyankhula za uchimo ndi kudya kwawo zinthu zoletsedwa? Ndithudi, zomwe akhala akuchitazo ndi zoipa zedi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek