×

Ndipo kumbukirani zabwino zimene Mulungu wakupatsani inu ndi lonjezo limene adakumangani nalo 5:7 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:7) ayat 7 in Chichewa

5:7 Surah Al-Ma’idah ayat 7 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 7 - المَائدة - Page - Juz 6

﴿وَٱذۡكُرُواْ نِعۡمَةَ ٱللَّهِ عَلَيۡكُمۡ وَمِيثَٰقَهُ ٱلَّذِي وَاثَقَكُم بِهِۦٓ إِذۡ قُلۡتُمۡ سَمِعۡنَا وَأَطَعۡنَاۖ وَٱتَّقُواْ ٱللَّهَۚ إِنَّ ٱللَّهَ عَلِيمُۢ بِذَاتِ ٱلصُّدُورِ ﴾
[المَائدة: 7]

Ndipo kumbukirani zabwino zimene Mulungu wakupatsani inu ndi lonjezo limene adakumangani nalo pamene inu mudanena kuti: “Tamva ndipo tidzatsatira.” Ndipo muopeni Mulungu. Ndithudi Iye amadziwa maganizo amene ali mu mtima mwanu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: واذكروا نعمة الله عليكم وميثاقه الذي واثقكم به إذ قلتم سمعنا وأطعنا, باللغة نيانجا

﴿واذكروا نعمة الله عليكم وميثاقه الذي واثقكم به إذ قلتم سمعنا وأطعنا﴾ [المَائدة: 7]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo kumbukirani chisomo cha Allah pa inu ndi pangano lake lomwe mudapangana Naye, pamene mudati: “Tamva, ndipo tamvera.” Muopeni Allah. Ndithudi Allah Ngodziwa za m’mitima
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek