×

Nena: “Inu anthu a m’Buku! Musaonjezere china chilichonse m’chipembedzo chanu chosakhala choonadi 5:77 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:77) ayat 77 in Chichewa

5:77 Surah Al-Ma’idah ayat 77 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 77 - المَائدة - Page - Juz 6

﴿قُلۡ يَٰٓأَهۡلَ ٱلۡكِتَٰبِ لَا تَغۡلُواْ فِي دِينِكُمۡ غَيۡرَ ٱلۡحَقِّ وَلَا تَتَّبِعُوٓاْ أَهۡوَآءَ قَوۡمٖ قَدۡ ضَلُّواْ مِن قَبۡلُ وَأَضَلُّواْ كَثِيرٗا وَضَلُّواْ عَن سَوَآءِ ٱلسَّبِيلِ ﴾
[المَائدة: 77]

Nena: “Inu anthu a m’Buku! Musaonjezere china chilichonse m’chipembedzo chanu chosakhala choonadi ndipo musatsatire zilakolako za anthu amene adasokera kale, amene anasocheretsa anthu ochuluka ndiponso adadzisocheretsa iwo eni kunjira yoyenera.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل ياأهل الكتاب لا تغلوا في دينكم غير الحق ولا تتبعوا أهواء, باللغة نيانجا

﴿قل ياأهل الكتاب لا تغلوا في دينكم غير الحق ولا تتبعوا أهواء﴾ [المَائدة: 77]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “E inu anthu a buku! Musapyole malire pa chipembedzo chanu popanda choonadi ndipo musatsatire zofuna za anthu omwe adasokera kale, nawasokeretsanso ambiri, ndi kusokera kunjira yowongoka (yolungama).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek