×

Ndithudi Ife tidamulenga munthu ndipo timadziwa zimene mtima wake umamuuza. Ndipo Ife 50:16 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Qaf ⮕ (50:16) ayat 16 in Chichewa

50:16 Surah Qaf ayat 16 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Qaf ayat 16 - قٓ - Page - Juz 26

﴿وَلَقَدۡ خَلَقۡنَا ٱلۡإِنسَٰنَ وَنَعۡلَمُ مَا تُوَسۡوِسُ بِهِۦ نَفۡسُهُۥۖ وَنَحۡنُ أَقۡرَبُ إِلَيۡهِ مِنۡ حَبۡلِ ٱلۡوَرِيدِ ﴾
[قٓ: 16]

Ndithudi Ife tidamulenga munthu ndipo timadziwa zimene mtima wake umamuuza. Ndipo Ife tili pafupi ndi iye kuposa mtsempha wa moyo wake

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولقد خلقنا الإنسان ونعلم ما توسوس به نفسه ونحن أقرب إليه من, باللغة نيانجا

﴿ولقد خلقنا الإنسان ونعلم ما توسوس به نفسه ونحن أقرب إليه من﴾ [قٓ: 16]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu tidamulenga munthu, ndipo Ife tikudziwa zimene mtima wake ukumunong’oneza; ndipo Ife tili pafupi ndi iye kuposa mtsempha wam’khosi mwake (wolumikizana ndi mtima)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek