×

(Ndipo kudzanenedwa kwa anthu ochimwa) kuti, “Ndithudi inu simudafune kuchenjezedwa za chimenechi 50:22 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Qaf ⮕ (50:22) ayat 22 in Chichewa

50:22 Surah Qaf ayat 22 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Qaf ayat 22 - قٓ - Page - Juz 26

﴿لَّقَدۡ كُنتَ فِي غَفۡلَةٖ مِّنۡ هَٰذَا فَكَشَفۡنَا عَنكَ غِطَآءَكَ فَبَصَرُكَ ٱلۡيَوۡمَ حَدِيدٞ ﴾
[قٓ: 22]

(Ndipo kudzanenedwa kwa anthu ochimwa) kuti, “Ndithudi inu simudafune kuchenjezedwa za chimenechi ndipotsopano Ifetavundukulachimenechimakuphimbani. Ndipo lero maso anu ali kuona zenizeni.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لقد كنت في غفلة من هذا فكشفنا عنك غطاءك فبصرك اليوم حديد, باللغة نيانجا

﴿لقد كنت في غفلة من هذا فكشفنا عنك غطاءك فبصرك اليوم حديد﴾ [قٓ: 22]

Khaled Ibrahim Betala
“(Adzauzidwa): “Ndithu udali wosalabadira zinthu izi; basi takuvundukulira (chomwe) chimakuphimba, ndipo kuyang’ana kwako lero nkwakuthwa!”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek