Quran with Chichewa translation - Surah Qaf ayat 23 - قٓ - Page - Juz 26
﴿وَقَالَ قَرِينُهُۥ هَٰذَا مَا لَدَيَّ عَتِيدٌ ﴾
[قٓ: 23]
﴿وقال قرينه هذا ما لدي عتيد﴾ [قٓ: 23]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (Mngelo) yemwe adali naye (pamodzi ndikumalemba zochita zake) adzanena (kwa Mngelo wachilango): “Izi ndizimene zidakonzedwa ndi ine.” |