Quran with Chichewa translation - Surah Qaf ayat 9 - قٓ - Page - Juz 26
﴿وَنَزَّلۡنَا مِنَ ٱلسَّمَآءِ مَآءٗ مُّبَٰرَكٗا فَأَنۢبَتۡنَا بِهِۦ جَنَّٰتٖ وَحَبَّ ٱلۡحَصِيدِ ﴾
[قٓ: 9]
﴿ونـزلنا من السماء ماء مباركا فأنبتنا به جنات وحب الحصيد﴾ [قٓ: 9]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo tatsitsa madzi odalitsidwa kuchokera ku mitambo, ndipo kupyolera m’madziwo, tameretsa (mmera) m’minda ndi mbewu zokololedwa |