Quran with Chichewa translation - Surah AT-Tur ayat 23 - الطُّور - Page - Juz 27
﴿يَتَنَٰزَعُونَ فِيهَا كَأۡسٗا لَّا لَغۡوٞ فِيهَا وَلَا تَأۡثِيمٞ ﴾
[الطُّور: 23]
﴿يتنازعون فيها كأسا لا لغو فيها ولا تأثيم﴾ [الطُّور: 23]
Khaled Ibrahim Betala “Azikalandirana m’menemo (mwachikondi wina ndi mnzake) chikho chodzaza ndi zakumwa; sipakakhala kwa iwo zolankhula zachabe ngakhale zochita zamachimo |