Quran with Chichewa translation - Surah AT-Tur ayat 37 - الطُّور - Page - Juz 27
﴿أَمۡ عِندَهُمۡ خَزَآئِنُ رَبِّكَ أَمۡ هُمُ ٱلۡمُصَۜيۡطِرُونَ ﴾
[الطُّور: 37]
﴿أم عندهم خزائن ربك أم هم المصيطرون﴾ [الطُّور: 37]
Khaled Ibrahim Betala “Kapena nkhokwe (za zabwino) za Mbuye wako zili ndi iwo (kotero kuti akuzigwiritsa ntchito mmene angafunire?) Kapena iwo ngopambana |