Quran with Chichewa translation - Surah An-Najm ayat 28 - النَّجم - Page - Juz 27
﴿وَمَا لَهُم بِهِۦ مِنۡ عِلۡمٍۖ إِن يَتَّبِعُونَ إِلَّا ٱلظَّنَّۖ وَإِنَّ ٱلظَّنَّ لَا يُغۡنِي مِنَ ٱلۡحَقِّ شَيۡـٔٗا ﴾
[النَّجم: 28]
﴿وما لهم به من علم إن يتبعون إلا الظن وإن الظن لا﴾ [النَّجم: 28]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo alibe kudziwa kulikonse pa zimenezo sakutsata china koma maganizo. Ndipo ndithu kuganizira sikuthandiza chilichonse pofuna kupeza choonadi |