Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qamar ayat 6 - القَمَر - Page - Juz 27
﴿فَتَوَلَّ عَنۡهُمۡۘ يَوۡمَ يَدۡعُ ٱلدَّاعِ إِلَىٰ شَيۡءٖ نُّكُرٍ ﴾
[القَمَر: 6]
﴿فتول عنهم يوم يدع الداع إلى شيء نكر﴾ [القَمَر: 6]
Khaled Ibrahim Betala “Choncho, apewe (iwe Mtumiki) osakhulupirira, (yembekezani) tsiku loitana woitana (wa Allah) ku chinthu chovuta kwambiri, (chodedwa ndi mitima) |