Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Rahman ayat 76 - الرَّحمٰن - Page - Juz 27
﴿مُتَّكِـِٔينَ عَلَىٰ رَفۡرَفٍ خُضۡرٖ وَعَبۡقَرِيٍّ حِسَانٖ ﴾
[الرَّحمٰن: 76]
﴿متكئين على رفرف خضر وعبقري حسان﴾ [الرَّحمٰن: 76]
Khaled Ibrahim Betala “Uku atatsamira misamiro yawofuwofu yokutidwa ndi zobiriwira; ndi zoyala zokongola, zakapangidwe kabwino |