×

Ndipo iwo amene amakhulupirira mwa Mulungu ndi mwa Mtumwi wake, iwo ndi 57:19 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hadid ⮕ (57:19) ayat 19 in Chichewa

57:19 Surah Al-hadid ayat 19 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hadid ayat 19 - الحدِيد - Page - Juz 27

﴿وَٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ بِٱللَّهِ وَرُسُلِهِۦٓ أُوْلَٰٓئِكَ هُمُ ٱلصِّدِّيقُونَۖ وَٱلشُّهَدَآءُ عِندَ رَبِّهِمۡ لَهُمۡ أَجۡرُهُمۡ وَنُورُهُمۡۖ وَٱلَّذِينَ كَفَرُواْ وَكَذَّبُواْ بِـَٔايَٰتِنَآ أُوْلَٰٓئِكَ أَصۡحَٰبُ ٱلۡجَحِيمِ ﴾
[الحدِيد: 19]

Ndipo iwo amene amakhulupirira mwa Mulungu ndi mwa Mtumwi wake, iwo ndi olungama ndi okhulupirira pamaso pa Ambuye wawo. Iwo adzalandira mphotho yawo pamodzi ndi muuni. Ndipo iwo amene sakhulupirira ndipo amakana chivumbulutso chathu, amenewa ndiwo a ku moto wa ku Gahena

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذين آمنوا بالله ورسله أولئك هم الصديقون والشهداء عند ربهم لهم أجرهم, باللغة نيانجا

﴿والذين آمنوا بالله ورسله أولئك هم الصديقون والشهداء عند ربهم لهم أجرهم﴾ [الحدِيد: 19]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo amene akhulupirira Allah ndi aneneri Ake, iwowo ndiwo owona (pa chikhulupiliro); ndi ofera pa njira ya Allah (onsewo) azapeza malipiro awo ndi kuwala kwawo kwa Mbuye wawo. Koma amene sadakhulupirire ndi kutsutsa zisonyezo zathu iwowo ndi eni a ku Jahena
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek