Quran with Chichewa translation - Surah Al-hadid ayat 28 - الحدِيد - Page - Juz 27
﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ ٱتَّقُواْ ٱللَّهَ وَءَامِنُواْ بِرَسُولِهِۦ يُؤۡتِكُمۡ كِفۡلَيۡنِ مِن رَّحۡمَتِهِۦ وَيَجۡعَل لَّكُمۡ نُورٗا تَمۡشُونَ بِهِۦ وَيَغۡفِرۡ لَكُمۡۚ وَٱللَّهُ غَفُورٞ رَّحِيمٞ ﴾
[الحدِيد: 28]
﴿ياأيها الذين آمنوا اتقوا الله وآمنوا برسوله يؤتكم كفلين من رحمته ويجعل﴾ [الحدِيد: 28]
Khaled Ibrahim Betala “E inu amene mwakhulupirira! Opani Allah, ndipo khulupirirani mthenga Wake, akupatsani zigawo ziwiri za chifundo Chake. Ndipo akupangirani kuunika koongoka nako (poyenda patsiku la chiweruziro.) Ndiponso akukhululukirani ndipo Allah Ngokhululuka mochuluka kwambiri, Ngwachisoni chosatha |