×

Misonkhano yamseri imachokera kwa Satana amene amafuna kusokoneza anthu okhulupirira. Koma Iye 58:10 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Mujadilah ⮕ (58:10) ayat 10 in Chichewa

58:10 Surah Al-Mujadilah ayat 10 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mujadilah ayat 10 - المُجَادلة - Page - Juz 28

﴿إِنَّمَا ٱلنَّجۡوَىٰ مِنَ ٱلشَّيۡطَٰنِ لِيَحۡزُنَ ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَلَيۡسَ بِضَآرِّهِمۡ شَيۡـًٔا إِلَّا بِإِذۡنِ ٱللَّهِۚ وَعَلَى ٱللَّهِ فَلۡيَتَوَكَّلِ ٱلۡمُؤۡمِنُونَ ﴾
[المُجَادلة: 10]

Misonkhano yamseri imachokera kwa Satana amene amafuna kusokoneza anthu okhulupirira. Koma Iye sangawalakwitse ayi kupatula ndi chilolezo cha Mulungu ndipo mwa Mulungu ndi momwe anthu okhulupirira ayenera kuika chikhulupiriro chawo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إنما النجوى من الشيطان ليحزن الذين آمنوا وليس بضارهم شيئا إلا بإذن, باللغة نيانجا

﴿إنما النجوى من الشيطان ليحزن الذين آمنوا وليس بضارهم شيئا إلا بإذن﴾ [المُجَادلة: 10]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu manong’onong’o oipa amachokera kwa satana kuti adandaulitse amene akhulupirira; koma sangawapweteke nawo chilichonse kupatula Allah atafuna ndipo okhulupirira atsamire kwa Allah Yekha, (asalabadire zonong’onezana zawo)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek