×

Kodi iwe suwaona amene amapalana ubwenzi ndi anthu amene adalandira mkwiyo wa 58:14 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Mujadilah ⮕ (58:14) ayat 14 in Chichewa

58:14 Surah Al-Mujadilah ayat 14 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mujadilah ayat 14 - المُجَادلة - Page - Juz 28

﴿۞ أَلَمۡ تَرَ إِلَى ٱلَّذِينَ تَوَلَّوۡاْ قَوۡمًا غَضِبَ ٱللَّهُ عَلَيۡهِم مَّا هُم مِّنكُمۡ وَلَا مِنۡهُمۡ وَيَحۡلِفُونَ عَلَى ٱلۡكَذِبِ وَهُمۡ يَعۡلَمُونَ ﴾
[المُجَادلة: 14]

Kodi iwe suwaona amene amapalana ubwenzi ndi anthu amene adalandira mkwiyo wa Mulungu? Iwo si a m’gulu lako kapena a mgulu lawo, ndipo iwo amalumbira zabodza pamene ali kudziwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ألم تر إلى الذين تولوا قوما غضب الله عليهم ما هم منكم, باللغة نيانجا

﴿ألم تر إلى الذين تولوا قوما غضب الله عليهم ما هم منكم﴾ [المُجَادلة: 14]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi sukuwaona amene apalana ubwenzi ndi anthu amene Allah wawakwiira; iwo sali mwa inu ndiponso sali mwa iwo. Ndipo akulumbira zabodza uku akudziwa (kuti limeneli ndibodza)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek